KOCHI YAMANYADO YOCHEPERAPO

Fomu yofunsira

Kochi yocheperapoyi ndi yaofuofu ndipo ikungodikira inu mukaone ndikuvomereza kuti apa panagona luso.Basiyi iliphuliphuli kuchitira umboni zaubwino wake.

Golden Dragon kochi ikundikira inu kuti mukayione ndikukatsimikiza zaubwino wake.

-Yonyezimira ndikungola mochitisa kaso-Basiyi imaposa mabasi ena chifukwa chamapangidwe ake amkati omwe amapangidwa mosala chilengedwe (eco-friendly).

-Maonekedwe amkati ndiake ake osafanana ndi basi ina ili yonse.

-Basiyi ili ndi makhotedwe ndi mayendedwecatsopano otchedwa ISG oxialParallel System.

-Imayenda mokhazikika ndiponso mwa mphamvu.

-imakhala ndi mipando makumi atatu ndi isano kunjzerapo wa woyendetsa.

-Katundu sasowa malo oyika chifukwa basiyi ili ndi malo ena apadera oyikapo katundu.

-Okwera basiyi ali ndi mwayi ogwiritsa ntchito Makita a internet (WIFI) komanso atha kutchaja mafoni awo ndi USB mubasi momwemo.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6857J12
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : L8540 × W2500 × H3300
  • Malo amatayala :
  • Mipando : 35
  • Maziziridwe a mkati : 28,000 Kcal/Hr
  • Wailesi : DVD Player with 17" LCD Monitor
  • Ingini : Cummins EQB210-20 - Diesel Engine
  • Mphavu ya ingine : 155Kw/2500rpm