MABASI OZUNGULIRA MTAUNI

Fomu yofunsira

Kukula kwa ma basi awa kumapangitsa kuti mkati mwake mukhale motakasuka ndiponso mowala. Basiyi ili ndi zitseko zazikulu zomwe zimathandiza kuti anthu athe ku kwera kapena ku tsika mosavuta panthawi yomwe iwo akufulumira.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6125J13C
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 12000×2500×3350
  • Malo amatayala : 6100 mm
  • Mipando : 122(34+2+1+85 Standing)122(34+2+1+85 Standing)
  • Maziziridwe a mkati : 30,000Kcal/hr
  • Wailesi : FM/AM Radio with Mp3 Player
  • Ingini : CUMMINS ISLe 310 31 - Diesel
  • Mphavu ya ingine : 228kW/2200rpm