MAZZOCCHIA LARGE SIZE COMPACTORS-MAC2NB

Fomu yofunsira

Single bladed rear-loading compactor-Mac 2NB ndi rear-loading compactor yomwe imakhala ndi container yotseka yonyamulira zinyalala

SINGLE-BLADED REAR-LOADING COMPACTOR

-Mac 2NB ndi makina omwe anakonzedwa moyenerana ndi ntchito yomwe amagwira

-Imakhala ndi single-bladed compacting unit yomwe imayenda pa ma  exterior upper tracks awiri komanso ma lower piston rods mouth

-Imatsitsa zinyalala pogwiritsa ntchito bulkhead yamkati

-Ili ndi hydraulic  system yomwe imagwiritsa ntchito mphamvu za magetsi

-Chipangizo chonyamulira ma bin chinapangidwa ndi mmene malamulo a bungwe la European Union  komanso mofanana ndi mmene makina onse a kampani ya Mazzocchia amapangidwira

-Control panel ya oyendetsa ili ndi screen ya touch yomwe imawonetsa mitundu yosiyanasiyana malinga ndi ntchito yomwe ikugwiridwa

-Hydraulic system imagwira ntchito kamba ka mphamvu za magetsi

-Ili ndi njira zovomerezeka zotetezera oyigwiritsa ntchito

 ZIPANGIZO/MITUNDU YA MAKINA ONYAMULA MA BIN

-Ma Bin lifter amayambira pa 120-1100 liters,2.5cbm bins,4.5 cbm komanso ma skips

-Rear footboards

-Setelite vehicles

المواصفات :

  • Volume of body : 20-25 mc
  • Chassis : 3 axles, medium-heavy line
  • MTT : 26 Ton