CHILLER-CWS MODUL

Fomu yofunsira

COMPACT AND POWERFUL

System ya Climma ya CWS MODUL ndiyodalirika pa nkhani yochita air-condition pa ma yacht kuchokera pa 60 footer kufikira pa super yachts ya 50 meteres kukwera mmwamba.Modular system yopangidwa mu stainless steel kuthandizira ma condesersn komanso ma manifolds a madzi amu Nyanja ya mchere komanso madzi a fresh kuwonetsetsa kuti ma Climma CWS  ndiwodalirika komanso opezeka mosavuta.

ABWINO KOMANSO ODALIRIKA

Ma microprocessor a Climma mu CWS centralized control box,amchityang`anira komanso kuwona ma parameter onse ofunikira a system pogwiritsa ntchito Modbus interface protocol pofunika kukulitsa performance komanso kudalilika kwa system. Ma CWS MODUL amapezekanso ndi ma inverter drivers. Ma water cooled inverter a Climma amachotseratu start current ndipo amachepetsa kalandiridwe ka CWS units kufika mpaka pa 305

INAPANGIDWA NDI KOLITE YAPAMWAMBA

Ma sea water condenser onse komanso ma  sea water circuit ndi ma manifolds adapangidwa mu marine-grade cupronickel kuti akhale ndi resistance yambiri ku sea water corrosion. Fresh water circuit inapangidwa mu copper komanso stainless steel ndipo compressor iliyonse imathandiziridwa pa anti-vibration mounts mu stainless steel framed housing.

Modular design imatanthauza kuti Climma CWS MODUL ndiyodalirika kwambiri malinga ndi momwe idapangidwira.Compressor iliyonse imadziyimira payokha ndipo imatheka kuchitidwa bypass kuchokera ku system ngati ndikofunika kutero;ndipo ikhozanso kuchotsedwa kuti ikonzedwe kusiya system yonse ikugwirabe ntchito bwino lomwe. Chimodzimodzinso ngati ndikofunikira,ma modules owonjezera akhonzanso kuwonjezeredwa ku ma system omwe alipo kale kuti awonjezere mphamvu za kaziziridwe ku system yonse.

Njira zonse za magetsi zinapangidwa kale,kusiya ma connections okhawo ofunikira kwambiri ku installation yomaliza. Module iliyonse komanso system yonse inayesedwa kale bwino lomwe pa mulingo wovomererezeka.

A TAILORED SPECIFICATION SUIT

Imapezeka kuchokera pa 72 000 kufikira pa 576 000 BTU/h ndi option ya reverse cycle kapena  kapena cool only,modular design imawonetsetsa kuti CWS system ikugwirizana ndi kakulidwe ka yacht kupereka BTU/h output yokwera kuchokera kumayendewe a pang`onopang`ono.

Ma frame akhoza kubweretsedwa pamodzi kuti apange ma racks monga momwe ayenera kukhalira ndipo ndikothekanso kusintha malo a sea water circuit. Ma frame akhoza kupentedwa kuti afanane ndi zipangizo zonse za mu engine room komanso space ya machine kuwonetsetsa kuti system ikuwoneka bwino mofanana ndi mmene imagwilira ntchito;ma frame akhozanso kutsekedwa ndi ma insulated panels. System ya CWS MODUL ikhozanso kukonzedwa posagwiritsa ntchito frame.

المواصفات :

  • Zopezeka : 160 - 780 kg
  • Kulemera : 653 - 704 mm
  • Kutalika : 810 - 2220 mm
  • Kaziziridwe : 21 - 253 kW