CWS DC INVERTER SERIE DC50

Fomu yofunsira

Climma DC Inverter chiller yatsopano idapangidwa mwamakono ndipo inapangidwa pogwiritsa ntchito upangiri omwe kampani yopanga makinawa yakhala nawo kwa zaka zoposa makumi anayi. DC chiller ya Climma imagwira ntchito chifukwa cha water cooled inverter yomwe imachepetsa mpamvu zofunikira ndi 50% kusiyana ndi ma traditional chillers.

KUSIYANA KWA MPHAMVU ZOTULUKA KUCHOKA KU AIR-CONDITIONING UNIT

DC Chiller yatsopano inapangidwa kuti idzigwira ntchito pa mulingo woyenerera potengera ndi kuchuluka kwa mphamvu zomwe ziri zofunikira.. Frequency compressor imasiyanitsa kabweredwe ka mphamvu kuchokera pa 10,000 kufika pa 50,000Btu.

WATER COOLED INVERTER COMPRESSOR

Imagwira bwino ntchito mmadzi,ma water cooled inverter a Climma amateteza compressor kunkhani ya kutentha komanso ku voltage yokwera zomwe zimachititsa kuti ikhazikitsidwe mu engine room mosafuna mpweya wina

CLIMA INTELLIGENT CONTROL

Maziziridwe komanso matenthedwe amathandiziridwa ndi Climma Intelligent Control unit (CIC) yomwe imagwiritsa ntchito configured algorithms pofuna kupereka kuthekera kokwanira

ECO MODE CLIMMA CWS DC SPECIFICHE

Climma DC chiller imapereka kuthekera kokwanira pogwiritsa ntchito ECO mode. ECO mode imachititsa kuti chiller idzigwira ntchito pokhapokha pomwe generetor  ikugwira ntchito kapena pamene ili pa doko ndi mphamvu zochepa

ECO MODECLIMMA CWS DC SPECIFICHE

Ma chiller a Climma DC amapereka kuthekera kokwanira pogwiritsa  ECO mode yapaderadera. Eco mode imathandiza kuti chiller igwire ntchito koma pokhapokha pomwe generator ikugwira ntchito ngakhalendo pomwe ili pa doko ndi mphamvu zochepa.

NO START LOAD

Climma DC chiller siyifunikira ma amps owonjezera kuti compressor igwire ntchito

المواصفات :

  • Zopezeka : 48 kg
  • Kulemera : 453 mm
  • Kutalika :
  • Kaziziridwe : 3 - 14 kW