CHILLER-CWS SOLO

Fomu yofunsira

Climma CWS SOLO,ndi system yamphamvu yomwe idapangidwira ma yatch kuti akhale ogwira ntchito bwinobwino.Imapezeka kuyambir pa 60.000 mpaka pa 144.000 BTU/h ndi compressor,reverse cycle ngati default ndipo imazima pokhapokha ikachitidwa demand,CWS SOLO ndiyoyenera pa ma yacht oyambira 55 feet kufikira pa 30 metres.

MPHAMVU

Climma CWS SOLO ndi system ya mphamvu yomwe inapangidwira ma yachts pofuna kuti akhale mu condition yabwino. Imapezeka kuyambir pa 60.000 mpaka pa 144.000 BTU/h ndi compressor,reverse cycle ngati default ndipo imazima pokhapokha ikachitidwa demand,CWS SOLO ndiyoyenera pa ma yacht oyambira 55 feet kufikira pa 30 metres.

COMPACT

Ku VECO timadziwa mulingo womwe ukufunika kuti zinthu zitheke,ndipo ichi mchifukwa chake ma design athu nthawi zonse amapangidwa pa ma system amphamvu kwambiri. Ma system a Climma CWS SOLO anapangidwa kuti akhale  apamwamba kwambiri.

KOLITE

Kamba koti Climma ili ndi ma control system monitors akeake imachititsa kuti ma parameters onse ofunikira a CWS SOLO aziwonedwa bwinobwino zomwe zimachititsa kuti performance yake ikhale yopambana.

Ma condenser a see water komanso ma associated sea water circuit komanso ma manifolds anapangidwa mu marine-grade cupronickel kuti azipereka resistance ku sea water corrosion.Fresh water circuit inapangidwa mu copper komanso mu zitsulo ndipo compressor imachitidwa support pa anti-vibration.

KUTHEKERA KWAKE

Ma CWS SOLO amapezekanso ndi ma inverter drivers. Kamba koti Climma ili ndi ma water cooled inverters akeake omwe amachotserstu ma start current ndipo amachepetsa katengedwe ka mphamvu ka CWS units yofikira mpaka pa 30%

المواصفات :

  • Zopezeka : 78 - 160 kg
  • Kulemera : 506 - 630 mm
  • Kutalika : 400 - 480 mm
  • Kaziziridwe : 17-35 kW