Iyi ndi generator yomwe inapangidwa mwaukadaulo ndipo kampani ya Kohler imapereka zinthu izi:
-Warrant ya chaka chimodzi
Mechanic governor
Skid and Vibration Isolators
Circuit breaker yayikulu
Radiator yayikulu
Makina oteteza kuti generator isawonongeke
Ndi ya Manual
ZOPEZEKA PA ALTERNATOR
12v charge alternator and starter
KAMWEDWE KA MAFUTA
100% load: 3.2 Lph
75% load: 2.7 Lph