LUXURY COACH BUS

Fomu yofunsira

Mtundu wa XML6125J12 ndi basi yopangidwa ndimaulemu apadera okhala ndimizere yokongola ndipo yopangidwa bwino.

Kutsogolo ndi kumboyo kwa  buasiyi kuli mizere yosalala yomwe imapangitsa kuti basiyi ikhale yokongola kwambiri.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6125J12
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 12000 × 2550 × 3690
  • Malo amatayala : 6000 mm
  • Mipando : 51 (49+1+1)
  • Maziziridwe a mkati : Songz 32,000Kcal/Hr
  • Wailesi : DVD Player with 2 Nos 22" & 19" LCD Monitors
  • Ingini : Cummins Diesel Engine -ISLe 340 30 Six Cylinder
  • Mphavu ya ingine : 250KW /2100rpm