Generator iyi ili ndi zinthu izi:
Ili ndi engine yamphamvu
50c ambient radiator
Ili ndi tank ya mafuta yabwino
Vibration isolators
Ili ndi airfilter yabwino
Ili ndi line breaker
Ili ndi battery komanso ma cable oyambira
Ili ndi ndi CPCB-certified sound enclosure
ZOPEZEKA PA ALTERNATOR
Ili ndi Alternator yabwino yomwe imafikira pa mulingo oyenerera wa padziko lonse monga BSEN 60034 komanso ena a BS5000,VDE 0530,NEMA,MG1-32,IEC34,CSA C22.2-100,AS 1359.Iyoyi ilinso ndi zipangizo zomwe zimayichititsa kutulutsa mphamvu zambiri.
KAMWEDWE KA MAFUTA