SINGLE-BLADED SODE-LOADING SINGLE-OPERATED COMPACTOR
-Side-loading single-operated compactor imakhala ndi container yosungira zinyalala yotseka komanso chonyamulira ma bin
-Makinawa ali ndikuthekera konyamula zinthu zambiri pakamodzi ndipo amatha kunyamula zinyalala zolimba, ma pepala,ma galasi,ma plastic ndi masamba
-Makinawa amathanso kusuntha kwa ka mtunda kakatali ndithu ma container oyenda komanso ongokhala
-Amagwiritsa ntchito mphamvu za magetsi
-LAT2 imapereka control panel yokhala ndi screen ya touch ya makono yomwe imathandiza makinawa kugwira ntchito mu mulingo omwe ayenera kugwilira.
-Alinso ndi double flat-screen TFT Monitor ndicholinga choti agwire ntchito pa malo aakulu
-Alinso ndi njira zotetezera owagwiritsa ntchito mosavuta zovomerezeka ndi Machinery Directive komanso ku UNI EN 1501-2
CHIDA KOMANSO MTUNDU WA MAKINA ONYAMULIRA MA BIN
-Makina onyamulira ma bin a ma container okhala ndi standard attachement yofika mpaka pa 3200 litres
-Integral Control System pa malo okhala dalaivala yomwe ilinso ndi colour monitor