MAZZOCHIA SMALL SIZE COMPACTORS-MINISTAR

Fomu yofunsira

Ministar Single-bladed Tipper Truck: Awa amapangidwa ndi chitslo ndipo amakhala otseka; Ali ndi single blade yomwe imagwira ntchito chifkwa cha ma hydraulic cylinder  ndipo imakhala bwino kunyamulira zinyalala, ma cardboard,ma plastic komanso compost.

Fratelli Mazzocchia inayamba kugwira ntchito mchaka cha 1967.

Kuchokera mu zaka za mma 70,kampaniyi yakhala ikugwira ntchito kwa zaka zoposa makumi anayi zomwe zayipatsa danga komanso ukadaulo  womwe umayithandiza kufikira zofuna za makasitomala ake pantchito yonyamula zinyalala pa dziko lonse.

Pofuna kupereka katund u wapamwamba, Kampani ya Fratelli Mazzocchia imapanga katundu wake malingana ndi zofuna za uni en iso9001(ed.2008) ndipo chilolezo chinaperekedwa mchaka cha 1998.

CUSTOMISATION

-Zipangizo zonyamula ma bin zogwiritsa ntchito magetsi

-Kunyamula ma bin pogwiritsa ntchito zipangizo za automatic

-Ma stabilizer unit a ma bin

-Chipangizo chonyamula matumba a zinyalala zomwe ndikuphatikizanso zonyamula ma bin

-Zipangizo zopezera komanso kuyesera

-Chipangizo chowonera momwe mitundu iyenera kukhalira komanso video camera

-Control panel komanso chosungira ndondomeko ya momwe ntchito yagwiridwira kapena momwe zinthu zikuyendera

ZIPANGIZO ZA STANDARD

-Zonyamulira ma bin zofika mpaka pa ma litres 1700

-Zotsitsira katundu kuyika mu galimoto zikuluzikulu

المواصفات :

  • Volume of body : 3,5-8 mc
  • Chassis : Two axles, light
  • MTT : From 2,2 to 8 Ton