Ma Tower Lights a Coelmo adapangidwa kuti azitha kugwira ntchito pa malo komanso mu nyengo iliyonse. Kamba koti adapangidwa ndi zipangizo zapamwamba, ma Tower Lights a Coelmo amakhala ndi mawalidwe ofanana ndipo amapilira mu nyengo zovuta
Ndiwodalirika mukapangidwe
Monga takamba kale, ma Tower Lights a Coelmo ndiwodalirika kamba koti mwa zina ali ndi ma stabiliser komanso adapangidwa moti akhoza kusinthidwa matalikidwe. Ma Tower a Coelmo oyima komanso oyendayenda samasintha ngakhale akumane ndi mphepo ya mphamvu. Wolemera kapena wopepuka, amapangidwa ndi chitsulo kapena ma aluminium telescopic poles omwe amatha kukhala a manual,hydraulic kapena pneumatic extension yomwe imatha kufika mpaka pa 12 mters. Ma Tower Lights amenewa amatha kuzungulira 360°ndipo kapangidwe ka nyali zake kakhoza kuphatikizidwa ndi mitundu yosiyanasiyana ya halogen,meta halide kapena led lamps potengera ndi momwe kuwala kukufunikira.
Ma Tower Lights a Coelmo akhoza kupezeka mmalo osiyanasiyana pogwiritsa ntchito njira zosiyanasiyananso
-Ma towing trailer oyenda pang’onopang’ono omwe ndioyenera mmalo amene mukumangidwa nyumba
-Ma towing trailer oyenda mwachangu ndi chilolezo choyenda mmisewu ikuluikulu
Standards Applied
-Control panel yokhala ndi voltmeter komanso hourmeter
-Chitetezo cha engine cha engine chomwe chimachititsa kuti engine idzizizimitsa yokha pressure ikachepa kapena engine ikatentha kwambiri
-Batile lopangidwa mommo lokhala ndi ma volts 12