Fomu yofunsira
Single bladed rear-loading compactor-Mac 2NB ndi rear-loading compactor yomwe imakhala ndi container yotseka yonyamulira zinyalala
SINGLE-BLADED REAR-LOADING COMPACTOR
-Mac 2NB ndi makina omwe anakonzedwa moyenerana ndi ntchito yomwe amagwira
-Imakhala ndi single-bladed compacting unit yomwe imayenda pa ma exterior upper tracks awiri komanso ma lower piston rods mouth
-Imatsitsa zinyalala pogwiritsa ntchito bulkhead yamkati
-Ili ndi hydraulic system yomwe imagwiritsa ntchito mphamvu za magetsi
-Chipangizo chonyamulira ma bin chinapangidwa ndi mmene malamulo a bungwe la European Union komanso mofanana ndi mmene makina onse a kampani ya Mazzocchia amapangidwira
-Control panel ya oyendetsa ili ndi screen ya touch yomwe imawonetsa mitundu yosiyanasiyana malinga ndi ntchito yomwe ikugwiridwa
-Hydraulic system imagwira ntchito kamba ka mphamvu za magetsi
-Ili ndi njira zovomerezeka zotetezera oyigwiritsa ntchito
ZIPANGIZO/MITUNDU YA MAKINA ONYAMULA MA BIN
-Ma Bin lifter amayambira pa 120-1100 liters,2.5cbm bins,4.5 cbm komanso ma skips
-Rear footboards
-Setelite vehicles