Aqua Matic 700-1

Fomu yofunsira

Aqua Matic  ndimakina omwe apangidwa mwa luso ndipo ndiyosavuta kugwiritsa ntchito nkusiyana ndimakina ena omwe alipo pa msika. Makina amene angofika pa msika a Aqua Matic apangidwa ndiluso la mtengo wapatali ndipo akhonza kugwira ntchito paokha osafuna kuthandizidwa ndi munthu.

Aqua Matic yapangidwa mwaluso ndipo ndiyovomerekezedwa ndi NMEA 2000 Remote, makinawa atha kungwiritsidwa ndimolingana ndi zinthu zonse zomwe  zinapangidwa mogwirizana ndi NME 2000.  

AUTOMATED FUNCTIONS

Kugwiritsa ntchito tachi sikilini kumapepusa ntchito kwa amene akugwiritsa ntchito ndi chifukwa ndi a otomatiki makina amatha kugwira ntchito paokha popanda NMEA 200 Remote Compaltibility

munthu.  Mphamvuya otomatiki imalora makinawa kuyeza mlingo wa madzi malinga ndi momwe munthu akufunira.  Aqua Matic imanthanso yenga madzi kwa sabata imodzi popanda munthu ndipo iyo imatha kuzizimitsa yokha panthawi yomwe yamaliza ntchito yake malinga ndi mlingo womwe ina patsidwa.

Mita yoonetsa ndondomeko (Meter/Monitor)

Mita yotcheredwa pa ola limodzi imathandiza kuonetsetsa kuti kuti zonse zikuyenda bwino ndipo imachepesa kuonongeka kwa makinawa.Manambala a digito pa Salinity Mita amaonetsa kuchuluka kweni kweni kwa mulingo wa madzi, iziti ndi zofunika kwambiri kwa onse akugwiritsa makinawa.

Mapampu (Pumps)

Mapampu opandidwa mwaukadaulo wapadera owonjezera mphavu yosefera madzi yomwe amakhala kwa nthawi yoposa ma ola 2000 asanapangidwe selevisi.

Palinso mwayi mwayi osankha malingana ndi makondedwe: Patented High pressure Quintiplex Axial Plunger Pump ndi pampu yomwe imayendera madzi basi ndipo sifuna kufewesedwa ndi oyilo kapenanso kufuna kusintha oyilo pakapita nthawi. Pampu imeneyi imakhala nthawi yokwana maola 8000 isanafunike kupangidwa selevisi. Pampuyi ndiopangidwa ndi luso kwambiri ndipo sipanga dzimbiri chifukwa imakhala ndi Duplex yomwe imalimbanda ndi dzimbiri kuposa 316 stainless steel. Magwiridwe ntchito a pampuyi ndiosavuta ndipo amapereka mtendere kwa mwini makinawa.

Imakhala ndi mphavu zambiri kuma sichita phokoso.

PAMPU IMABWERA NDI IZI (ACCESSORIES)

Rimoti yokhala ndi tachi sikilini ya kala

Malinga nd makondedwe ogula atha kusankha Soft Motor Starter pa single phase AC imene imachepetsa mphavu ya magetsi yomwe imabwera poyasa makinawa ndi 60%.

Sefa ya Sea Strainer yokhala pa mtetete imakhalanso ndi Monel Mesh screen yosavuta kupuputa ndiponso sefayi imateteza mibulu kuundana.

Zinthu zina ngati Charcoal Filter Assembly, Commercial prefilter, Oil water separator, pH Neutralizer komanso AtuomaticFresh Flush zimabwera ndi pampuyi malingana ndikukonda kwa munthu.

Pampuyi imagwira ntchito mogwirizana ndi NMEA 200 (NMEA 2000 Compatibility)

Mutha kusankha kuti ipangidwe mogwiriza ndi NMEA 2000 kapena ayi

Itha kubwera ndi sikilini yowonerapo ndipo muthanso kuyiyasa angakhalenso kuyizimitsa ndi pogwiritsa sikiliniyi.

Mukafunanso imatha kubwera ndi NMEA rimoti control yokhala ndi sikilini.

Zida (Materials)

Makinawa amakhala ndi heve dute Magnetic Latching Relays (mphavu ya nyesi) yothandiza mota ikamazungulira.

Amabweranso ndi 316 Stainless Steel Pressure Transducers yosachita dzimbiri yomwe imawerengera ndikulemba momwe makina akugwirira ntchito.

Kuteteza (Safety)

Ili ndi Product Water Diversion Valve yomwe imapatutsa madzi.

Imagwira ntchito ndi mphavu yochepa ya magetsi zomwe zimateteza anthu ogwiritsa ntchito makinawa.

Malo onse amene amatulutsa mphavu yochuluka ndiokutidwa bwino kuopeza anthu kugwidwa shoko.

Serevisi ndimakonzedwe (Service and Maintenance)

Makina a Aqua Matic amatumizidwa kuchokera ku fakitole kuti inu oyigula mungowalumikiza ndikuyamba kuwagwiritsa ntchito.

Iwowa amabwera ndi ndondomeko yonse yamomwe mungalumikizire pa bukhu la magwiritsidwe.

Pamakhalanso kufutokoza pazomwe mungachite pamene mufuna chithandizo kwina kuli konse pano padziko lapansi.

المواصفات :

  • Zopezeka :
  • Mapangidwe : 29 gal / 110 lit per hour, 700 gal / 2,650 lit per day
  • Kulemera : 156 lbs / 71 Kg