Awa ndi ma Generator enanso a mphamvu omwe ali ndi ma engine omwe amathanso kudziziziritsa okha Ali ndi Thanki ya mafuta yabwino Vibration isolators Ma air filter abwino
Generator iyi ili ndi zinthu izi: Ili ndi engine yamphamvu 50c ambient radiator Ili ndi tank ya mafuta yabwino Vibration isolators Ili ndi airfilter yabwino
Ndiyapamwamba kwambiri komanso ili ndi ndi engine ya dizilo ya 12-volt battery charging alternator Ili ndi radiator yomwe imafikira pa 45°C (113°F) Thanki ya mafuta yabwino Vibration isolators
Inapangidwa mwaukadaula ndipo ili ndi engine ya dizilo yomwe ili ndi12-volt battery charging alternator 45° C ambient radiator Thanki ya mafuta Ma Isolator Ma Air filter
Kampani ya KOHLER imayika zofunikira zones pa Generatot-yi yomwe ili nso ndi engine ya dizilo ya 12-volt battery charging alternator Ili ambient radiator yomwe imafikira pa 45°C Thanki ya mafuta ya Subbase
Ndiyodalirika komanso ili ndi engine ya dizilo ya mphamvu kwambiri Ili ndi 45°C (113°F) ambient radiator. Thanki ya mafuta yabwino Dry type air filter Line breaker Batile komanso ma cable oyambira
Pa Generator iyi a KOHLER amapereka: Warrant ya chaka chimodzi Main line circuit breaker Radiator yokhalanso ndi chokupizira mpweya Grille yothandiza kuti ,idzigwira bwino ntchito
Monga ma Generator onse a kampani ya KOHLER, KD 165 inayesedwa kale bwino ku fakitale ndipo kampani-yi imapererkenso Warrant ya chaka chimodzi.
Ma Generator a kampani ya KOHLER Co ndi amphamvu kwambiri omwe anayesedwa mokwanira pa kagwiridwe kake ka ntchito.